

All of a sudden pa msika wa ma phone pangodzadza ma Samsung galaxy A17 and A 16 muti zukhala bwanj ?
reddit.comApapa nde it's a sign kuti pakhomo pamakolo paja tichoke hahahah chipinda chija chufunika chikhale warehouse 😢 😭 😄
Found this and laughed out loud ,😆 Mafana omwe akumakwanitsa kuwonela ma world cup games a 3AM ndi omwe amagona pa sitting room nyumba za ku Naperi, Soche East, Nkolokosa ndi Chitawira basi
Dear Microsoft, Our African names are not spelling errors.
reddit.comDear Microsoft, Our African names are not spelling errors.
reddit.comAmalawi tinadumpha mkodzo ndikuponda bibitu.mu zaka ziwiri za ulamuliro anthu adayamba kusimba lokoma.
Zinthu zosayiwalika ku Area 25 ndipo mwina ena sadziwa.
(1)Ku 25A mkati mwa msika mudali filling station yogulitsirapo paraffin
(2)Ku mchenga ku B mkatikati mwa manyumba muja muli toilet ya boma imene olo anthu ena okhala komweko sadziwa.Toilet imeneyi idamangidwa mu ulamuliro wa Bakiki Muluzi pa nthawi imene amafuna kumanga youth centre pamalopa koma anthu adadya ndalama zake.
(3)Galimoto imene amkakwera mtsogoleri wakale Bakili Muluzi munthawi imeneyo idapatsidwa kwa bambo Baisi amene amakhala ku 25 ndipo tikhulupilira kuti tidzitsulo tina mutha kukatipeza kunyumba ya bambo Baisi.
(3)Munthu amene adali wamphamvu kwambiri ndipo akalankhula anthu amachita mantha mu 25 yonse adali Malemu a Mbera aku 25A
(4)Anthu ambiri sadziwa kuti tchalitchi ya Zambezi pafupi ndi mzikiti wa 25B idamangidwa pa Manda ndipo manyumba onse ozungulira pamene paja ndithu nawomso adamangidwa pa Manda.
(5)Mu nthawi imeneyo,munthu amene amakatengedwa olemera kwambiri ku 25C lidali banja la Osman
(6)Malo onse a Zibweze komanso Nangamtani founder wake ndi bwana Pande.
(7)Asing'anga otchuka kwambiri ku 25C adali bambo Ngumbi
Is it too early to say Amalawi anavota mwazeru koma anavotera ma bulutu??
reddit.comPeople who don’t drink and smoke, how do you manage stress pa malawi pano ? Ndamva pa Galiva pali buy three get one for free tu.
reddit.comFound this 😆 😂 🤣 koma ndizoona izi?
ku Lilongwe ngongole imayambila pa 100 pin. Anything less, timangogailana lol.
THE K250, One ounce Gold Coin in 1978. Only 850 sold at K850 each.
In 1978 the reserve Bank issued a one ounce gold coin. The K250 coin showing Kamuzu on the face and a Nyala on the reverse. Cash price was 850 kwacha. Only 538 were sold apparently.
Today 13th May 2026..using the gold spot price and the prevailing bank rate this coin is worth over 8.5 million Kwacha.
Using Street value now 18 million.
Quite an increase in 48 years.