u/Writer265

▲ 12 r/Malawi

So on this 'adulting thing'

Ndekuto mafupawa and nsanawu uzipweteka moyo wako onse? Kapena zikumakhala bwanji kuntundako?

29M.

reddit.com
u/Writer265 — 2 days ago
▲ 10 r/Malawi

Links for business forums

Is there a subreddit for business stuff for malawians?

Chifukwa ma opportunity nde alipo, ndipo tikumayesela kuika pano , koma zikumatengedwa ngati ma scam, or an advertisement or even misleading..

Ine nde ndatopa nsaname

-

reddit.com
u/Writer265 — 17 days ago